2 Ndipo anatsegula pa dzenje la phompho; ndipo unakwera utsi woturuka m'dzenjemo, ngati utsi wa ng'anjo yaikuru; ndipo dzuwa ndi thambo zinada, cifukwa ca utsiwo wa kudzenje,
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9
Onani Cibvumbulutso 9:2 nkhani