Cibvumbulutso 9:5 BL92

5 Ndipo anapatsa ilo mphamvu si kuti likawaphe, komatu kuti likawazunze miyezi isanu; ndipo mazunzidwe ao anali ngati mazunzidwe a cinkhanira, pamene ciluma munthu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:5 nkhani