6 Ndipo m'masiku ajawo, anthu adzafunafuna imfa osaipeza konse; ndipo adzakhumba kumwalira, koma imfa idzawathawa.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9
Onani Cibvumbulutso 9:6 nkhani