Yohane 1:14 BL92

14 Ndipo Mau anasandulika thupi, nakhazikika pakati pa ife, ndipo tinaona ulemerero wace, ulemerero wonga wa wobadwa yekha wa Atate, wodzala ndi cisomo ndi coonadi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 1

Onani Yohane 1:14 nkhani