Yohane 1:15 BL92

15 Yohane acita umboni za iye, napfuula nati, Uyu ndiye amene ndinanena za iye, Wakudzayo pambuyo panga analipo ndisanabadwe ine; cifukwa anakhala woyamba wa ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 1

Onani Yohane 1:15 nkhani