Yohane 10:40 BL92

40 Ndipo anacoka kunkanso tsidya lija la Yordano, kumalo kumene kunali Yohane analikubatiza poyamba paja; ndipo anakhala komweko.

Werengani mutu wathunthu Yohane 10

Onani Yohane 10:40 nkhani