41 Ndipo ambiri anadza kwa iye; nanena kuti, Sanacita cizindikilo Yohane; koma zinthu ziri zonse Yohane ananena za iye zinali zoona.
Werengani mutu wathunthu Yohane 10
Onani Yohane 10:41 nkhani