Yohane 11:1 BL92

1 Koma panali munthu wodwala, Lazaro wa ku Betaniya, wa m'mudzi wa Mariya ndi mbale wace Marita.

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:1 nkhani