2 Koma ndiye Mariya uja anadzoza Ambuye ndi mafuta onunkhira bwino, napukuta mapazi ace ndi tsitsi lace, amene mlongo wace Lazaro anadwala.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:2 nkhani