Yohane 11:31 BL92

31 Pamenepo Ayuda okhala naye m'nyumba, ndi kumtonthoza iye, pakuona Mariya ananyamuka msanga, naturuka, namtsata iye, ndi kuyesa kuti amuka kumanda kukalira komweko.

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:31 nkhani