32 Pomwepo Mariya, pofika pamene panali Yesu, m'mene anamuona iye, anagwa pa mapazi ace, nanena ndi iye, Ambuye, mukadakhala kuno Inu, mlongo wanga sakadamwalira.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:32 nkhani