41 Pomwepo anacotsa mwala. Kama Yesu anakweza maso ace kupenya kumwamba nati, Atate, ndiyamika Inu kuti munamva Ine.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:41 nkhani