42 Koma ndadziwa Ine kuti mumandimva Ine nthawi zonse; koma cifukwa ca khamu la anthu alikuimirira pozungulira ndinanena ici, kuti akhulupire kuti Inu munandituma Ine.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:42 nkhani