Yohane 11:56 BL92

56 Pamenepo analikumfuna Yesu, nanena wina ndi mnzace poimirira iwo m'Kacisi, Muyesa bwanji inu, sadzadza kuphwando kodi?

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:56 nkhani