Yohane 11:57 BL92

57 Koma ansembe akulu ndi Afarisi adalamulira, kuti, munthu wina akadziwa pokhala iye, aulule, kuti akamgwire iye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:57 nkhani