13 anatenga makwata a kanjedza, naturuka kukakomana ndi iye, napfuula, Hosana; wolemekezeka iye wakudza m'dzina la Ambuye, ndiye Mfumu ya Israyeli.
Werengani mutu wathunthu Yohane 12
Onani Yohane 12:13 nkhani