Yohane 14:11 BL92

11 Khulupirirani Ine, kuti Inendiri mwa Atate ndi Atate ali mwa Ine; koma ngati si comweco, khulupirirani Ine cifukwa ca nchito zomwe.

Werengani mutu wathunthu Yohane 14

Onani Yohane 14:11 nkhani