10 Ngati musunga malamulo anga mudzakhala m'cikondi canga; monga Ine ndasunga malamulo a Atate wanga, ndipo ndikhala m'cikondi cace.
Werengani mutu wathunthu Yohane 15
Onani Yohane 15:10 nkhani