Yohane 16:23 BL92

23 Ndipo tsiku limenelo simudzandifunsa kanthu. Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Ngati mudzapempha Atate kanthu, adzakupatsani inu m'dzina langa.

Werengani mutu wathunthu Yohane 16

Onani Yohane 16:23 nkhani