33 Zinthu izi ndalankhula ndi inu, kuti mwa Ine mukakhale nao mtendere. M'dziko lapansi mudzakhala naco cibvuto, koma limbikani mtima; ndalilaka dziko lapansi Ine.
Werengani mutu wathunthu Yohane 16
Onani Yohane 16:33 nkhani