1 Zinthu izi analankhula Yesu; ndipo m'mene anakweza maso ace Kumwamba, anati, Atate, yafika nthawi; lemekezani Mwana wanu, kuti Mwana wanu akulemekezeoi Inu;
Werengani mutu wathunthu Yohane 17
Onani Yohane 17:1 nkhani