Yohane 18:16 BL92

16 koma Petro anaima kukhomo kunja, Cifukwa cace wophunzira winayo amene anadziwika kwa mkulu wa ansembe, anaturuka nalankhula ndi wapakhomo, nalowetsa Petro.

Werengani mutu wathunthu Yohane 18

Onani Yohane 18:16 nkhani