Yohane 19:10 BL92

10 Cifukwa cace Pilato ananena kwa iye, Simulankhula ndi ine kodi? simudziwa kodi kuti ulamuliro ndiri nao wakukumasulani, ndipo ndiri nao ulamuliro wakukupacikani?

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:10 nkhani