Yohane 19:14 BL92

14 Koma linali tsiku lokonza Paskha; panali monga ora lacisanu ndi cimodzi. Ndipo ananena kwa Ayuda, Taonani, Mfumu yanu!

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:14 nkhani