Yohane 19:20 BL92

20 Ndipo lembo ilo analiwerenga ambiri a Ayuda; cifukwa malo amene Yesu anapaeikidwapo anali pafupipa mudziwo; ndipo linalembedwa m'Cihebri, ndi m'Ciroma, ndi m'Cihelene.

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:20 nkhani