Yohane 19:34 BL92

34 koma mmodzi wa asilikari anamgwaza ndi nthungo m'nthiti yace, ndipo 2 panaturuka pomwepo mwazi ndi madzi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:34 nkhani