Yohane 19:35 BL92

35 Ndipo 3 iye amene anaona, wacita umboni, ndi umboni wace uti woona; ndipo iyeyu adziwa kuti anena zoona, kuti inunso mukakhulupire.

Werengani mutu wathunthu Yohane 19

Onani Yohane 19:35 nkhani