Yohane 2:10 BL92

10 nanena naye, Munthu ali yense amayamba kuika vinyo wokoma; ndipo anthu atamwatu, pamenepo wina wosakoma; koma iwe wasunga vinyo wokoma kufikira tsopano lino.

Werengani mutu wathunthu Yohane 2

Onani Yohane 2:10 nkhani