11 Ciyambi ici ca zizindikilo zace Yesu anacita m'Kana wa m'Galileya naonetsera ulemerero wace; ndipo akuphunzira ace anakhulupirira iye.
Werengani mutu wathunthu Yohane 2
Onani Yohane 2:11 nkhani