Yohane 20:1 BL92

1 Koma tsiku loyamba la Sabata anadza Mariya wa Magadala mamawa, kusanayambe kuca, kumanda, napenya mwala wocotsedwa kumanda.

Werengani mutu wathunthu Yohane 20

Onani Yohane 20:1 nkhani