2 Pomwepo anathamanga nadza kwa Simoni Petro ndi kwa wophunzira wina amene Yesu anamkonda, nanena nao, Anacotsa Ambuye kumanda, ndipo sitidziwa kumene anamuika iye.
Werengani mutu wathunthu Yohane 20
Onani Yohane 20:2 nkhani