Yohane 20:19 BL92

19 Pamenepo, pokhala madzulo, tsiku lomwelo, loyamba la Sabata, makomo ali citsekere, kumene anakhala akuphunzira, cifukwa ca kuopa Ayuda, Yesu anadza naimirira pakati pao, nanena nao, Mtendere ukhale ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 20

Onani Yohane 20:19 nkhani