Yohane 20:20 BL92

20 Ndipo pamene adanena ici, anaonetsa iwo manja ace ndi nthiti zace. Pamenepo akuphunzira anakondwera pakuona Ambuye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 20

Onani Yohane 20:20 nkhani