Yohane 21:8 BL92

8 Koma akuphunzira ena anadza m'kangalawa, pakuti sanali kutali ndi mtunda, koma monga mikono mazana awiri, nakoka khoka la nsombazo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 21

Onani Yohane 21:8 nkhani