Yohane 3:18 BL92

18 Wokhulupirira Iye saweruzidwa; wosakhulupira waweruzidwa ngakhale tsopano, cifukwa sanakhulupirira dzina la Mwana wobadwa yekha wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:18 nkhani