19 Koma ciweruziro ndi ici, kuti kuunika kunadza ku dziko lapansi, ndipo anthu anakonda mdima koposa kuunika; pakuti nchito zao zinali zoipa.
Werengani mutu wathunthu Yohane 3
Onani Yohane 3:19 nkhani