Yohane 3:3 BL92

3 Yesu anayankha nati kwa iye, Indetu, indetu, ndinena ndi iwe, Ngati munthu sabadwa mwatsopano, sakhoza kuona Ufumu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 3

Onani Yohane 3:3 nkhani