Yohane 4:46 BL92

46 Cifukwa cace Yesu anadzanso ku Kana wa m'Galileya, kumene anasandutsa madzi vinyo. Ndipo kunalimkulu wina wa mfumu, mwana wace anadwala m'Kapernao.

Werengani mutu wathunthu Yohane 4

Onani Yohane 4:46 nkhani