Yohane 4:47 BL92

47 Iyeyu, pamene anamva kuti Yesu wacokera ku Yudeya nafika ku Galileya, ananka kwa iye, nampempha kuti atsike kukaciritsa mwana wace; pakuti anali pafupi imfa.

Werengani mutu wathunthu Yohane 4

Onani Yohane 4:47 nkhani