Yohane 5:21 BL92

21 Pakuti monga Atate aukitsa akufa, nawapatsa moyo, momwemonso Mwanaapatsa moyo iwo amene iye afuna.

Werengani mutu wathunthu Yohane 5

Onani Yohane 5:21 nkhani