Yohane 5:20 BL92

20 Pakuti Atate akonda Mwana, namuonetsa zonse azicita yekha: ndipo adzamuonetsa nchito zoposa izi, kuti mukazizwe,

Werengani mutu wathunthu Yohane 5

Onani Yohane 5:20 nkhani