Yohane 5:32 BL92

32 Wocita umboni wa Ine ndi wina; ndipo ndidziwa kuti umboni umene iye andicitira Ine uli woona.

Werengani mutu wathunthu Yohane 5

Onani Yohane 5:32 nkhani