Yohane 5:6 BL92

6 Yesu, pakuona ameneyo alikugona, ndipo anadziwa kuti anatero nthawi yaikuru pamenepo, ananena naye, Ufuna kuciritsidwa kodi?

Werengani mutu wathunthu Yohane 5

Onani Yohane 5:6 nkhani