Yohane 6:11 BL92

11 Pomwepo Yesu anatenga mikateyo; ndipo pamene adayamika, anagawira iwo akukhala pansi; momwemonso ndi tinsomba, monga momwe iwo anafuna.

Werengani mutu wathunthu Yohane 6

Onani Yohane 6:11 nkhani