Yohane 8:10 BL92

10 Koma Yesu pamene adaweramuka, anati kwa iye, Mkazi iwe, ali kuti ajawa? Palibe munthu anakutsutsa kodi?

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:10 nkhani