18 Ine ndine wakucita umboni wa Ine ndekha, ndipo Atate amene anandituma Ine, acita umboni wa Ine.
Werengani mutu wathunthu Yohane 8
Onani Yohane 8:18 nkhani