19 Cifukwa cace ananena ndi iye, Ali kuti Atate, wanu? Yesu anayankha, Simudziwa kapena Ine, kapena Atate wanga; mukadadziwa Ine, mukada-dziwanso Atate wanga.
Werengani mutu wathunthu Yohane 8
Onani Yohane 8:19 nkhani