Yohane 8:33 BL92

33 Anamyankha iye, Tiri mbeu ya Abrahamu, ndipo sitinakhala akapolo a munthu nthawi iri yonse; munena bwanji; Mudzayesedwa aufulu?

Werengani mutu wathunthu Yohane 8

Onani Yohane 8:33 nkhani