41 Inu mucita nchito za atate wanu. Anati kwa iye, Sitinabadwa ife m'cigololo; tiri naye Atate mmodzi ndiye Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Yohane 8
Onani Yohane 8:41 nkhani