17 Pamenepo ananenanso kwa wosaonayo, Iwe unenanji za iye, popeza anakutsegulira maso ako? Koma iye anati, Ali Mneneri.
Werengani mutu wathunthu Yohane 9
Onani Yohane 9:17 nkhani